Mtonga Isaac Pharmacy Online

-->
Skip to main contentMtonga Isaac Pharmacy is Health and Medical facility that manufacture Herbal medicines at Traditional level and provides treatment to so many kinds of diseases. This Health facility is based on Herbal medicines rather than Drugs to maintain good health. It is branded by Dr. Mtonga N. Isaac (Herbalist) in Lusaka capital city of Zambia, African region. This business name was registered on 23rd March, 2022 according to Act No: 16 of 2011 of the Laws of Zambia.
Mwambi umenewu umanenedwa pa mlandu ngati anthu awiri atengana mlandu ndi kuyamba kutsutsana. Monga tidziwa mlandu uliwonse sulephera amene wauutsa poti mnzache apsye mtima.
Chotero akamakangana, wina kukanira mnzache kuti sindinayambe ine, koma wangonditenga pa mlanduwu popanda kuchimwa, pompo anthu ndi pamene amanena mwambi umenewu kufanizira kuthyoka mnyanga kwa njobvu. Ponena mau otero.
Zonenedwa pa mirandu amati anthu ayambe kuona amene wautsa nkhaniyo poti atengerane kubwalo. Nthano ya mwambi uwu ndi iyi:
*Kale-kale anthu ananka ku uzimba kukapha nyama. Anthu aja alikusaka nyama anatulukira pomwe njobvu itafa patsinde pa mtengo wa dzaye, mnyanga wache umodzi utathyoka.
Anthu ena nati, "Taonani njobvu yathyoka mnyanga ndi dzaye."
Ena anayankha nati, "Muzinena, 'Chatsitsa dzayelo m'mwambamo poti njobvu ithyoke mnyanga'." Anthu aja pofuna-funa kuti aone chimene chatsitsa dzaye mu mtengo, anapeza kuti anali Bwampini amene anali kufuna kudya dzaye; pokwera m'mwambamo anapulumutsira dzaye pansi pamene panagona njobvu ndi kuthyoka mnyanga wache.
Nchimodzi-modzi ndi mlandu umakhala ndi yemwe wayamba kuchimwa poti atengerane anthu kubwalo la milandu.
KONKHANI MIYAMBI YINA MUSIMU
______________________________________________________________
Contact us:
Mtonga Isaac Pharmacy,
Ng'ombe Township,
#16/24 Off Zambezi road,
Email: mtongaisaacpharmacy@gmail.com,
Tel: +260974272433/+260966399444,
Lusaka, Zambia.
_______________________________________ _______________________________________